Mafunso Ndi Mayankho, Vol. 1: Mulungu Ndi Chilengedwe
- 1
Mlungu Ndi Ndani? - 2
Analenga Mulungu Ndani? - 3
Kodi Mulungu Ali Ndi Chiyambi? - 4
Kodi Mulungu Angathe Kufa? - 5
Kodi Kulinso Mulungu Wina? - 6
Mulungu M’modzi Apezeka Kangati? - 7
Mulungu Mwa Atatu Ndi Ndani? - 8
Mulungu Ali Kuti? - 9
Mungaone Mlungu? - 10
Kodi Mulungu Adziwa Zonse? - 11
Kodi Mulungu Angathe Zonse? - 12
Anakulenga Ndani? - 13
Anakulengeranji Mulungu? - 14
Ndi Chaninso Chomwe Mulungu Analenga? - 15
Mulungu Analengeranji Zonsezi? - 16
Ungatamande Bwanji Mlungu? - 17
Chifukwa Chani Ndilemekeze Mlungu? - 18
Makolo Athu Oyamba Ndani? - 19
Mulungu Anawumba Bwanji Adamu Ndi Hava? - 20
Anapereka Chiani Mulungu Kwa Adamu Ndi Hava Pamwamba Pa Thupi? - 21
Kodi Uli Ndi Mzimu Ndiponso Thupi? - 22
Kodi Adamu Ndi Hava Mulungu Anawalenga Otani?
2016 Dana Dirksen


